Numeri 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Benjamini anali Abidana,+ mwana wa Gidiyoni.