Numeri 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wansembe azidzapereka nsembe yophimba tchimo la munthu amene walakwa pochimwira Yehova mosazindikira, ndipo adzakhululukidwa.+
28 Wansembe azidzapereka nsembe yophimba tchimo la munthu amene walakwa pochimwira Yehova mosazindikira, ndipo adzakhululukidwa.+