Numeri 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wansembe apereke nsembe yophimba tchimo la munthuyo, amene walakwira Yehova mosazindikira, kuti akhululukidwe.+
28 Wansembe apereke nsembe yophimba tchimo la munthuyo, amene walakwira Yehova mosazindikira, kuti akhululukidwe.+