-
Numeri 18:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Gawo limene muzilandira lizichokera pa nsembe zonse zopatulika koposa zowotcha pamoto. Nsembe zake ndi izi: nsembe zilizonse zimene angapereke kwa ine, kuphatikizapo nsembe zawo zambewu,+ nsembe zawo zamachimo+ komanso nsembe zawo zakupalamula.+ Gawolo lizikhala chinthu chopatulika koposa kwa iwe ndi ana ako.
-