-
Numeri 18:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Ndipo uwauze kuti, ‘Mukapereka zabwino koposa za zoperekazo, Mulungu aziona kuti Alevinu mwapereka tirigu wochokera pamalo opunthira, vinyo wochokera mopondera mphesa kapena mafuta ochokera mʼchofinyira mafuta.
-