Numeri 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Ndipo uwauze kuti, ‘Mukapereka zabwino koposa za zoperekazo,+ zotsalazo zizikhala za Alevinu, monga tirigu wochokera popunthira, vinyo wochokera mopondera mphesa, kapena mafuta ochokera m’chofinyira mafuta.
30 “Ndipo uwauze kuti, ‘Mukapereka zabwino koposa za zoperekazo,+ zotsalazo zizikhala za Alevinu, monga tirigu wochokera popunthira, vinyo wochokera mopondera mphesa, kapena mafuta ochokera m’chofinyira mafuta.