Numeri 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho iwo anayamba kudandaula motsutsana ndi Mulungu komanso Mose+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani munatitulutsa mʼdziko la Iguputo kuti tidzafere mʼchipululu muno? Kuno kulibe chakudya komanso madzi,+ ndipo chakudya chonyansachi chafika potikola.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:5 Nsanja ya Olonda,8/15/1999, ptsa. 26-27
5 Choncho iwo anayamba kudandaula motsutsana ndi Mulungu komanso Mose+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani munatitulutsa mʼdziko la Iguputo kuti tidzafere mʼchipululu muno? Kuno kulibe chakudya komanso madzi,+ ndipo chakudya chonyansachi chafika potikola.”+