Numeri 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nthawi yomweyo Mose anapanga njoka yakopa+ nʼkuiika pamtengo.+ Ndiye munthu akalumidwa ndi njoka nʼkuyangʼana njoka yakopayo, ankakhalabe ndi moyo.+
9 Nthawi yomweyo Mose anapanga njoka yakopa+ nʼkuiika pamtengo.+ Ndiye munthu akalumidwa ndi njoka nʼkuyangʼana njoka yakopayo, ankakhalabe ndi moyo.+