Numeri 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Amowabuwo anauza akuluakulu a ku Midiyani+ kuti: “Chigulu cha anthuchi chidzadya malo athu onse ngati mmene ngʼombe imadyera msipu kubusa.” Pa nthawi imeneyo, Balaki mwana wa Zipori ndi amene anali mfumu ya Mowabu.
4 Choncho Amowabuwo anauza akuluakulu a ku Midiyani+ kuti: “Chigulu cha anthuchi chidzadya malo athu onse ngati mmene ngʼombe imadyera msipu kubusa.” Pa nthawi imeneyo, Balaki mwana wa Zipori ndi amene anali mfumu ya Mowabu.