-
Numeri 22:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma Mulungu ataona kuti Balamu akupita, anapsa mtima ndipo mngelo wa Yehova anaima pamsewu kuti amutchingire njira. Balamuyo anali atakwera bulu wake, ndipo anali ndi anyamata ake awiri.
-