Numeri 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Mulungu anapsa mtima poona kuti Balamu akupita, moti mngelo wa Yehova anaima pamsewu kuti amutchingire njira.+ Balamuyo anali pabulu wake, ndipo anali ndi anyamata ake awiri. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:22 Nsanja ya Olonda,8/1/2004, tsa. 27
22 Tsopano Mulungu anapsa mtima poona kuti Balamu akupita, moti mngelo wa Yehova anaima pamsewu kuti amutchingire njira.+ Balamuyo anali pabulu wake, ndipo anali ndi anyamata ake awiri.