-
Numeri 22:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Kenako mngelo wa Yehovayo anakaima panjira yopanikiza imene inali pakati pa minda iwiri ya mpesa ndipo njirayo inali ndi khoma lamiyala uku ndi uku.
-