-
Numeri 22:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Mngelo wa Yehovayo anakaimanso panjira yopanikiza yodutsa pakati pa minda ya mpesa. Njirayo inali ndi khoma la miyala uku ndi uku.
-