-
Numeri 22:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Tsopano mngelo wa Yehova anasunthiranso patsogolo nʼkukaima pamalo ena opanikiza, pomwe panalibiretu mpata woti nʼkudutsira kudzanja lamanja kapena lamanzere.
-