-
Numeri 22:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Buluyo anafunsanso Balamu kuti: “Kodi si ine bulu wanu amene mwakhala mukukwera moyo wanu wonse mpaka lero? Kodi ndinayamba ndachitapo zimenezi kwa inu?” Iye anayankha kuti: “Ayi!”
-