Numeri 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Buluyo anafunsanso Balamu kuti: “Kodi si ine bulu wanu amene mwakhala mukukwera moyo wanu wonse mpaka lero? Kodi ndinayamba ndachitapo zimenezi kwa inu?”+ Iye anayankha kuti: “Iyayi!”
30 Buluyo anafunsanso Balamu kuti: “Kodi si ine bulu wanu amene mwakhala mukukwera moyo wanu wonse mpaka lero? Kodi ndinayamba ndachitapo zimenezi kwa inu?”+ Iye anayankha kuti: “Iyayi!”