Numeri 22:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Buluyu anandiona ndipo anayesa kundipatukira maulendo atatu onsewa.+ Akanapanda kundipatukira, bwenzi pano nʼtakupha. Koma buluyu nʼkanamusiya kuti akhale ndi moyo.”
33 Buluyu anandiona ndipo anayesa kundipatukira maulendo atatu onsewa.+ Akanapanda kundipatukira, bwenzi pano nʼtakupha. Koma buluyu nʼkanamusiya kuti akhale ndi moyo.”