Numeri 22:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma buluyu wandiona, ndipo wayesa kundipewa maulendo atatu onsewa.+ Akanapanda kundipewa, ndithu, bwenzi pano n’takupha.+ Koma buluyu n’kanamusiya kuti akhale ndi moyo.”
33 Koma buluyu wandiona, ndipo wayesa kundipewa maulendo atatu onsewa.+ Akanapanda kundipewa, ndithu, bwenzi pano n’takupha.+ Koma buluyu n’kanamusiya kuti akhale ndi moyo.”