Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 22:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno buluyo anaona mngelo wa Yehova ali chilili pamsewu lupanga lake lili m’manja.+ Pamenepo buluyo anayesetsa kupatukira kumbali kwa msewu kuti adutse kutchire, koma Balamu anayamba kum’kwapula kuti am’bwezere mumsewu.

  • Numeri 22:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Buluyo anaonanso mngelo wa Yehova uja. Ndipo anayamba kudzikanikizira kukhoma, moti anakanikiziranso phazi la Balamu kukhomako. Pamenepo, Balamu anayamba kum’kwapulanso kwambiri bulu uja.

  • Numeri 22:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Buluyo ataonanso mngelo wa Yehova, tsopano anangokhala pansi, Balamu ali pamsana pake. Pamenepo Balamu anapsa mtima koopsa,+ ndipo anayamba kum’kwapulanso ndi ndodo yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena