-
Numeri 22:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Balamu anauza mngelo wa Yehovayo kuti: “Ndachimwa, sindinadziwe kuti inuyo munaima pamsewu kudzakumana nane. Koma ngati sizinakusangalatseni, ndikhoza kubwerera.”
-