Numeri 22:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Balamu atamva zimenezi anauza mngelo wa Yehovayo kuti: “Ndachimwa,+ sindinadziwe kuti inuyo munaima pamsewu kudzakumana nane. Bwanji ndibwerere ngati sizinakusangalatseni?”
34 Balamu atamva zimenezi anauza mngelo wa Yehovayo kuti: “Ndachimwa,+ sindinadziwe kuti inuyo munaima pamsewu kudzakumana nane. Bwanji ndibwerere ngati sizinakusangalatseni?”