-
Numeri 22:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Balaki atamva kuti Balamu wafika, nthawi yomweyo ananyamuka kukamulandira kumzinda wa Mowabu. Mzindawu uli mʼmbali mwa mtsinje wa Arinoni, umene uli mʼmalire a dzikolo.
-