Numeri 22:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Balaki atamva kuti Balamu wafika, nthawi yomweyo ananyamuka kukamulandira kumzinda wa Mowabu. Mzindawu unali pafupi ndi mtsinje wa Arinoni, umene unali kumalire a dzikolo.+
36 Balaki atamva kuti Balamu wafika, nthawi yomweyo ananyamuka kukamulandira kumzinda wa Mowabu. Mzindawu unali pafupi ndi mtsinje wa Arinoni, umene unali kumalire a dzikolo.+