Numeri 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Balaki anauza Balamu kuti: “Chonde tabwerani. Tiyeni tipite kumalo enanso. Mwina kumeneko Mulungu woona angalole kuti mutemberere anthuwa.”+
27 Balaki anauza Balamu kuti: “Chonde tabwerani. Tiyeni tipite kumalo enanso. Mwina kumeneko Mulungu woona angalole kuti mutemberere anthuwa.”+