Numeri 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Balaki anauza Balamu kuti: “Chonde tabwerani. Tiyeni tipite kumalo enanso. Mwina kumeneko Mulungu woona angalole kuti munditembererere anthuwa.”+
27 Koma Balaki anauza Balamu kuti: “Chonde tabwerani. Tiyeni tipite kumalo enanso. Mwina kumeneko Mulungu woona angalole kuti munditembererere anthuwa.”+