Numeri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Balamu ataona kuti Yehova akufuna* kudalitsa Aisiraeli, sanapitenso kukafunafuna njira yoti awalodzere,+ mʼmalomwake anayangʼana kuchipululu.
24 Balamu ataona kuti Yehova akufuna* kudalitsa Aisiraeli, sanapitenso kukafunafuna njira yoti awalodzere,+ mʼmalomwake anayangʼana kuchipululu.