Numeri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Balamu ataona kuti Yehova akungowadalitsa Aisiraeli, sanapitenso kukawafunira tsoka lina lililonse+ mmene anachitira nthawi zina zija.+ M’malomwake, anatembenuka n’kuyang’ana kuchipululu.
24 Balamu ataona kuti Yehova akungowadalitsa Aisiraeli, sanapitenso kukawafunira tsoka lina lililonse+ mmene anachitira nthawi zina zija.+ M’malomwake, anatembenuka n’kuyang’ana kuchipululu.