Genesis 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+ Levitiko 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Musadye chilichonse limodzi ndi magazi.+ “‘Musaombeze*+ ndipo musachite zamatsenga.+ Numeri 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Palibe amene walodza Yakobo,+Ngakhale kuchesa Isiraeli.+Za Yakobo ndi Isiraeli, adzati,‘Mwaonatu zimene Mulungu wachita!’+
27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+
23 Palibe amene walodza Yakobo,+Ngakhale kuchesa Isiraeli.+Za Yakobo ndi Isiraeli, adzati,‘Mwaonatu zimene Mulungu wachita!’+