Numeri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula Aisiraeli kuti, ‘Muzionetsetsa kuti mukupereka kwa ine nsembe yanga, yomwe ndi chakudya changa. Pa nthawi yake yoikidwiratu muzipereka nsembe zanga zowotcha pamoto, kuti zikhale kafungo kosangalatsa* kwa ine.’+
2 “Lamula Aisiraeli kuti, ‘Muzionetsetsa kuti mukupereka kwa ine nsembe yanga, yomwe ndi chakudya changa. Pa nthawi yake yoikidwiratu muzipereka nsembe zanga zowotcha pamoto, kuti zikhale kafungo kosangalatsa* kwa ine.’+