Numeri 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imeneyi ndi nsembe yopsereza ya tsiku la Sabata, ndipo muziipereka nthawi zonse limodzi ndi nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku komanso nsembe yake yachakumwa.+
10 Imeneyi ndi nsembe yopsereza ya tsiku la Sabata, ndipo muziipereka nthawi zonse limodzi ndi nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku komanso nsembe yake yachakumwa.+