Numeri 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imeneyi ndi nsembe yopsereza ya tsiku lasabata, yoperekedwa pa tsiku la sabata lililonse. Muziipereka limodzi ndi nsembe yopsereza+ ya tsiku ndi tsiku, pamodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+
10 Imeneyi ndi nsembe yopsereza ya tsiku lasabata, yoperekedwa pa tsiku la sabata lililonse. Muziipereka limodzi ndi nsembe yopsereza+ ya tsiku ndi tsiku, pamodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+