Numeri 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Muzipereka nsembe yopsereza yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova. Muzipereka ngʼombe ziwiri zazingʼono zamphongo, nkhosa imodzi yamphongo ndi ana a nkhosa 7 amphongo, achaka chimodzi.+
27 Muzipereka nsembe yopsereza yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova. Muzipereka ngʼombe ziwiri zazingʼono zamphongo, nkhosa imodzi yamphongo ndi ana a nkhosa 7 amphongo, achaka chimodzi.+