Numeri 28:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Muzipereka zimenezi kuwonjezera pa nsembe yanu yopsereza ya nthawi zonse ndi nsembe yake yambewu. Muzionetsetsa kuti nyamazo nʼzopanda chilema+ ndipo muzipereka limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.’”
31 Muzipereka zimenezi kuwonjezera pa nsembe yanu yopsereza ya nthawi zonse ndi nsembe yake yambewu. Muzionetsetsa kuti nyamazo nʼzopanda chilema+ ndipo muzipereka limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.’”