Numeri 28:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Muzipereka zimenezi+ kuwonjezera pa nsembe yanu yopsereza ya tsiku ndi tsiku ndi nsembe yake yambewu. Muzionetsetsa kuti nyamazo n’zopanda chilema.+ Muziperekanso nsembe yake yachakumwa.+
31 Muzipereka zimenezi+ kuwonjezera pa nsembe yanu yopsereza ya tsiku ndi tsiku ndi nsembe yake yambewu. Muzionetsetsa kuti nyamazo n’zopanda chilema.+ Muziperekanso nsembe yake yachakumwa.+