Numeri 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+ Numeri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muzipereka nsembezi limodzi ndi ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,+ monga nsembe yambewu.+ Ufawo muziuthira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini.+ Numeri 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Muzipereka nsembe zimenezi, kuwonjezera pa nsembe yopsereza+ ya m’mawa ya tsiku ndi tsiku.+
3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+
5 Muzipereka nsembezi limodzi ndi ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,+ monga nsembe yambewu.+ Ufawo muziuthira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini.+