Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+

  • Levitiko 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Lamula Aroni ndi ana ake kuti, ‘Lamulo la nsembe yopsereza+ lili motere: Nsembe yopsereza izikhala pamoto, paguwa lansembe, usiku wonse kufikira m’mawa, ndipo moto wa paguwapo uzisonkhezeredwa.

  • Numeri 29:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo.+ Muzim’pereka kuwonjezera pa nsembe yamachimo pa tsiku lophimba machimo, ndi nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe zake zambewu ndiponso zachakumwa.+

  • Ezekieli 46:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 M’mawa uliwonse, iwo azipereka kwa ansembe mwana wa nkhosa wamphongo, nsembe yambewu ndi mafuta, kuti zikhale nsembe yopsereza yathunthu ya nthawi zonse.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena