Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 28:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+

  • Danieli 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iyo inadzitama kwambiri mpaka kukafika kwa Kalonga wa khamulo.+ Inalanda Kalongayu nsembe yoyenera kuperekedwa nthawi zonse,+ ndipo malo opatulika amene iye anakhazikitsa anagwetsedwa.+

  • Danieli 11:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno padzauka magulu ankhondo* otuluka mwa iye. Maguluwo adzaipitsa malo opatulika+ amene ndi malo okhala ndi mpanda wolimba kwambiri, ndipo adzachotsa nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse.+

      “Iwo adzaika pamalowo chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko.+

  • Danieli 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwa,+ ndiponso pamene chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwa, padzapita masiku 1,290.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena