-
Numeri 29:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Muziperekanso ufa wosalala wothira mafuta monga nsembe zake zambewu. Ufawo uzikhala wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa pa ngʼombe yamphongoyo, magawo awiri mwa magawo 10 pa nkhosa yamphongoyo
-