Numeri 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muziperekanso ufa wosalala wothira mafuta monga nsembe zake zambewu. Ufawo uzikhala wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa pang’ombe yamphongoyo, magawo awiri mwa magawo 10 pankhosa yamphongoyo,+
3 Muziperekanso ufa wosalala wothira mafuta monga nsembe zake zambewu. Ufawo uzikhala wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa pang’ombe yamphongoyo, magawo awiri mwa magawo 10 pankhosa yamphongoyo,+