Numeri 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa tsiku lachiwiri, muzipereka ngʼombe 12 zazingʼono zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, zonse zizikhala zopanda chilema.+
17 Pa tsiku lachiwiri, muzipereka ngʼombe 12 zazingʼono zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, zonse zizikhala zopanda chilema.+