Numeri 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Pa tsiku lachiwiri, muzipereka ng’ombe 12 zazing’ono zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+
17 “‘Pa tsiku lachiwiri, muzipereka ng’ombe 12 zazing’ono zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+