Numeri 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atanyamuka ku Etamu anabwerera mʼmbuyo kulowera ku Pihahiroti amene anali moyangʼanizana ndi Baala-zefoni.+ Ndipo anakamanga msasa pafupi ndi Migidoli.+
7 Atanyamuka ku Etamu anabwerera mʼmbuyo kulowera ku Pihahiroti amene anali moyangʼanizana ndi Baala-zefoni.+ Ndipo anakamanga msasa pafupi ndi Migidoli.+