Numeri 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atanyamuka ku Etamu anabwerera m’mbuyo kulowera ku Pihahiroti.+ Pihahiroti anali moyang’anana ndi Baala-zefoni.+ Ndipo anakamanga msasa pafupi ndi Migidoli.+
7 Atanyamuka ku Etamu anabwerera m’mbuyo kulowera ku Pihahiroti.+ Pihahiroti anali moyang’anana ndi Baala-zefoni.+ Ndipo anakamanga msasa pafupi ndi Migidoli.+