Numeri 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mutenge mtsogoleri mmodzi pa fuko lililonse kuti akathandize kugawa malowo kuti akhale cholowa chanu.+
18 Mutenge mtsogoleri mmodzi pa fuko lililonse kuti akathandize kugawa malowo kuti akhale cholowa chanu.+