Numeri 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mukapereke kwa Alevi mizinda 6 yoti munthu amene wapha mnzake azikathawirako. Kuwonjezera pa mizindayi, mukapereke kwa Aleviwo mizinda ina 42.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2140
6 Mukapereke kwa Alevi mizinda 6 yoti munthu amene wapha mnzake azikathawirako. Kuwonjezera pa mizindayi, mukapereke kwa Aleviwo mizinda ina 42.+