Numeri 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Mukapatse Alevi mizinda 6 yoti munthu amene wapha mnzake azikathawirako.+ Kuwonjezera pa mizindayi, mukapatse Aleviwo mizinda ina 42. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2140
6 “Mukapatse Alevi mizinda 6 yoti munthu amene wapha mnzake azikathawirako.+ Kuwonjezera pa mizindayi, mukapatse Aleviwo mizinda ina 42.