Numeri 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, mʼdziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:14 Mawu a Mulungu, ptsa. 92-94
14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, mʼdziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako.