Numeri 35:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Musamadetse dziko limene mukukhalamo, limene inenso ndikukhalamo, chifukwa ine Yehova ndikukhala pakati pa Aisiraeli.’”+
34 Musamadetse dziko limene mukukhalamo, limene inenso ndikukhalamo, chifukwa ine Yehova ndikukhala pakati pa Aisiraeli.’”+