Deuteronomo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndiyeno tinatembenuka nʼkulowera kuchipululu kudzera njira ya ku Nyanja Yofiira, mogwirizana ndi zimene Yehova anandiuza.+ Ndipo tinayenda masiku ambiri mʼdera lapafupi ndi phiri la Seiri.
2 “Ndiyeno tinatembenuka nʼkulowera kuchipululu kudzera njira ya ku Nyanja Yofiira, mogwirizana ndi zimene Yehova anandiuza.+ Ndipo tinayenda masiku ambiri mʼdera lapafupi ndi phiri la Seiri.