Deuteronomo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndiyeno tinatembenuka ndi kulowera kuchipululu kudzera njira ya ku Nyanja Yofiira, monga mmene Yehova anandiuzira.+ Ndipo tinayenda masiku ambiri m’dera lapafupi ndi phiri la Seiri.
2 “Ndiyeno tinatembenuka ndi kulowera kuchipululu kudzera njira ya ku Nyanja Yofiira, monga mmene Yehova anandiuzira.+ Ndipo tinayenda masiku ambiri m’dera lapafupi ndi phiri la Seiri.